1 Chronicles 1:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kusi adabereka Nimirodi. Iyeyu ndiye adayamba kukhala munthu wamphamvu pa dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Kusi anabala Nimirodi; iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu kwambiri pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Kusi anabala Nimmdi; iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko.