1 Chronicles 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kanani adabereka Sidoni mwana wake wachisamba ndi Heti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Kanani anabala Sidoni mwana wake woyamba, ndi Heti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni, ndipo anaberekanso Ahiti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Kanani anabala Zidoni mwana wace woyamba, ndi Heti,