1 Chronicles 1:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ebere adabereka ana aamuna aŵiri. Mwana wina anali Pelegi (pakuti anthu adaagaŵikana pa nthaŵi yake), ndipo mbale wake anali Yokotani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Eberi anabala ana amuna awiri, dzina la winayo ndiye Pelegi, popeza masiku ake dziko linagawanika; ndi dzina la mbale wake ndiye Yokotani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Eberi anabereka ana aamuna awiri: wina anamutcha Pelegi, chifukwa pa nthawiyo anthu a pa dziko lapansi anagawikana. Dzina la mʼbale wake linali Yokitani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Eberi anabala ana amuna awiri, dzina la winayo ndiye Pelegi, popeza masiku ace dziko linagawanika; ndi dzina la mbale wace ndiye Yokitani.