1 Chronicles 1:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onseŵa anali ana a Yokotani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabu. Awa onse ndiwo ana a Yokotani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabi. Awa onse ndiwo ana a Yokitani.