1 Chronicles 1:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mibadwo yao nayi: mwana wachisamba wa Ismaele anali Nebayoti. Panalinso Kedara, Adibeele, Mibisamu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismaele Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeele, ndi Mibisamu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu zake zinali izi: Nebayoti ndiye anali mwana woyamba wa Ismaeli, kenaka Kedara, Adibeeli, Mibisamu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mibadwo yao ndi awa; woyamba wa Ismayeli Nebayoti; ndi Kedara ndi Adibeli, ndi Mibisamu,