1 Chronicles 1:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu naŵa: Zimirani, Yokosamu, Medani, Midiyani, Isibaki, ndiponso Suwa. Ana a Yokosamu naŵa: Sheba ndi Dedani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimirani, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midiyani, ndi Isibaki, ndi Suwa. Ndi ana a Yokisani: Sheba, ndi Dedani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu anali awa: Zimurani, Yokisani, Medani, Midiyani, Isibaki ndi Suwa. Ana a Yokisani ndi awa: Seba ndi Dedani
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimiramu, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midyani, ndi Isibaki, ndi Sua. Ndi ana a Yokisani: Seba, ndi Dedani.