1 Chronicles 1:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Sobala naŵa: Aliyani, Manahati, Ebala, Sefi ndi Onamu. Ana a Zibiyoni naŵa: Aiya ndi Ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Sobala: Aliyani, ndi Manahati, ndi Ebala, Sefi, ndi Onamu. Ndi ana a Zibiyoni: Aiya ndi Ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Sobala anali awa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu. Ana aamuna a Zibeoni anali awa: Ayiwa ndi Ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Sobala: Abiani, ndi Manahati, ndi Ebala, Sefi, ndi Oramu. Ndi ana a Zibeoni: Aiya ndi Ana.