1 Chronicles 1:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni naŵa: Hamurani, Esibani, Itirani, ndi Kerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamurani, ndi Esibani, ndi Itirani, ndi Kerani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni anali awa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamirani, ndi Esibani, ndi Itrani, ndi Kerani.