1 Chronicles 1:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Ezere naŵa: Bilihani, Zaavani ndi Yaakani. Ana a Disani naŵa: Uzi ndi Arani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Ezere: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Yaakani. Ana a Disani: Uzi, ndi Arani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Ezeri anali awa: Bilihani, Zaavani ndi Yaakani. Ana aamuna a Disani anali awa: Uzi ndi Arani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Ezeri: Bilani, ndi Zavani, ndi Yakani. Ana a Disani: Uzi, ndi Arani.