1 Chronicles 1:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Husamu atafa, Hadadi mwana wa Bedadi, amene adagonjetsa Amidiyani ku dziko la Mowabu, adaloŵa ufumu m'malo mwake. Mzinda wake ankautchula kuti Aviti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwalira Husamu; ndi Hadadi mwana wa Bedadi, amene anakantha Midiyani ku thengo la Mowabu, anakhala mfumu m'malo mwake; ndi dzina la mudzi wake ndi Aviti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdziko la Mowabu, analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Aviti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwalira Husamu; ndi Hadada mwana wa Bedadi, amene anakantha Midyani ku thengo la Moabu, anakhala mfumu m'malo mwace; ndi dzina la mudzi wace ndi Aviti.