1 Chronicles 1:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hadadi atafa, Samila wa ku Masireka adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwalira Hadadi; ndi Samila wa ku Masireka anakhala mfumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwalira Hadada; ndi Samla wa ku Masereka anakhala mfumu m'malo mwace.