1 Chronicles 1:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samila atafa, Shaulo wa ku Rehoboti ku Yufurate, adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwalira Samila: ndi Shaulo wa ku Rehoboti ku nyanja anakhala mfumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwalira Samla: ndi Sauli wa ku Rehoboti ku nyanja anakhala mfumu m'malo mwace.