1 Chronicles 1:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Shaulo atafa, Baala-Hanani mwana wa Akibori adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwalira Shaulo; ndi Baala-Hanani mwana wa Akibori anakhala mfumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli atamwalira, Baala-Hanani mwana wa Akibori analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwalira Sauli; ndi Baalahanani mwana wa Akiboro anakhala mfumu m'malo mwace.