1 Chronicles 1:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Kusi naŵa: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka. Ana a Raama naŵa: Sheba ndi Dedani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka. Ndi ana a Raama: Sheba, ndi Dedani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Kusi anali: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka Ana aamuna a Raama anali: Seba ndi Dedani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Rama, ndi Sabteka. Ndi ana a Rama: Seba, ndi Dedani.