1 Chronicles 10:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
amuna onse olimba mtima adanyamuka kukatenga mtembo wa Saulo ndi mitembo ya ana ake kubwera nayo ku Yabesi. Adakwirira mafupa aowo patsinde pa mtengo wa thundu ku Yabesi, ndipo adasala zakudya masiku asanu ndi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anauka ngwazi zonse, nachotsa mtembo wa Saulo, ndi mitembo ya ana ake, nabwera nayo ku Yabesi, naika mafupa ao patsinde pa mtengo wathundu ku Yabesi, nasala masiku asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anthu awo onse olimba mtima anapita kukatenga mitembo ya Sauli ndi ana ake ndipo anabwera nayo ku Yabesi. Anakwirira mafupa awo pansi pa mtengo wabwemba ku Yabesi, ndipo anasala kudya masiku asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
anauka ngwazi zonse, nacotsa mtembo wa Sauli, ndi mitembo ya ana ace, nabwera nayo ku Yabesi, naika mafupa ao patsinde pa mtengo wathundu ku Yabesi, nasala masiku asanu ndi awiri.