1 Chronicles 10:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo sankafuna kuti Chauta amutsogolere. Nchifukwa chake Chautayo adamupha napereka ufumu kwa Davide mwana wa Yese.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osafunsira kwa Yehova; chifukwa chake anamupha, napambutsira ufumu kwa Davide mwana wa Yese.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
sanafunsire nzeruzo kwa Yehova. Choncho Yehova anamupha ndi kupereka ufumu kwa Davide mwana wa Yese.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osafunsira kwa Yehova; cifukwa cace anamupha, napambutsira ufumu kwa Davide mwana wa Jese.