1 Chronicles 10:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Afilistiwo adapanikiza Saulo ndi ana ake, ndipo adapha Yonatani, Abinadabu ndi Malikisuwa ana a Saulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Afilisti anaumirira kutsata Saulo ndi ana ake, ndi Afilistiwo anawapha Yonatani, ndi Abinadabu, ndi Malikisuwa, ana a Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Afilisti anapanikiza kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo anapha Yonatani, Abinadabu ndi Maliki-Suwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Afilisti anaumirira kutsata Sauli ndi ana ace, ndi Afilistiwo anawapha Yonatani, ndi Abinadabu, ndi Malikisuwa, ana a Sauli.