1 Chronicles 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wonyamula zida uja ataona kuti Sauloyo wafa, nayenso adadzigwetsa pa lupanga lake, nkufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene wonyamula zida zake anaona kuti Saulo wafa, anagwera nayenso lupanga lake, nafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mnyamata wonyamula zida zake uja ataona kuti Sauli wafa, nayenso anadzigwetsera pa lupanga lake nafa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene wonyamula zida zace anaona kuti Sauli wafa, anagwera nayenso lupanga lace, nafa.