1 Chronicles 11:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina atatu mwa atsogoleri makumi atatu aja adatsikira ku thanthwe mpaka kwa Davide ku phanga la Adulamu. Kufupi nkumeneko ankhondo a Afilisti anali atamanga zithando zankhondo ku chigwa cha Refaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatu a akulu makumi atatu anatsikira kuthanthwe kwa Davide, ku phanga la Adulamu; ndi nkhondo ya Afilisti idamanga misasa m'chigwa cha Refaimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atatu mwa atsogoleri makumi atatu aja anabwera kwa Davide ku thanthwe ku phanga la Adulamu pamene gulu la Afilisti linali litamanga misasa mʼchigwa cha Refaimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atatu a akuru makumi atatu anatsikira kuthanthwe kwa Davide, ku phanga la Adulamu; ndi nkhondo ya Afilisti idamanga misasa m'cigwa ca Refaimu.