1 Chronicles 11:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amphamvu a m'magulu ankhondowo anali aŵa: Asahele mbale wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amphamvuwo a magulu a nkhondo ndiwo Asahele mbale wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankhondo amphamvuwa anali: Asaheli mʼbale wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amphamvuwo a magulu a nkhondo ndiwo Asaheli mbale wa Yoabu, Elanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,