1 Chronicles 11:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zeloki Mwamoni, Naharai wa ku Beeroti, wonyamula zida za Yowabu mwana wa Zeruya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zeleki Mwamoni, Naharai Mbeeroti wonyamula zida za Yowabu mwana wa Zeruya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zeleki Mwamoni, Naharai wa ku Beeroti, mnyamata wonyamula zida za Yowabu mwana wa Zeruya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zeleki M-amoni, Naharai Mberoti wonyamula zida za Yoabu mwana wa Zeruya,