1 Chronicles 11:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Davide pamodzi ndi Aisraele onse adapita kukathira nkhondo mzinda wa Yerusalemu, ndiye kuti Yebusi, kumene kunkakhala Ayebusi nzika za dzikolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namuka Davide ndi Aisraele onse naye ku Yerusalemu, ndiwo Yebusi; ndipo Ayebusi nzika za m'dziko zinali komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide ndi Aisraeli onse anapita ku Yerusalemu (ku Yebusi). Ayebusi amene ankakhala kumeneko
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namuka Davide ndi Aisrayeli onse naye ku Yerusalemu, ndiwo Yebusi; ndipo Ayebusi nzika za m'dziko zinali komweko.