1 Chronicles 11:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adina mwana wa Siza Mrubeni, mtsogoleri wa Arubeni, ndi anthu makumi atatu pamodzi naye,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adina mwana wa Siza Mrubeni mkulu wa Arubeni, ndi makumi atatu pamodzi naye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adina mwana wa Siza Mrubeni, amene anali mtsogoleri wa Arubeni ndi anthu makumi atatu pamodzi naye,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adina mwana wa Siza Mrubeni mkuru wa Arubeni, ndi makumi atatu pamodzi naye,