1 Chronicles 11:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti Davide ankakhala m'lingamo, lingalo linkatchedwa Mzinda wa Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakhala m'lingamo; chifukwa chake analitcha mudzi wa Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Davide anakhazikika mu lingamo, ndipo mzindawu anawutcha Mzinda wa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakhala m'lingamo; cifukwa cace analicha mudzi wa Davide.