1 Chronicles 11:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adamanga mzinda kuzungulira deralo kuyambira ku linga la Milo mpaka m'kati mwake. Yowabu ndiye adakonza mbali ina ya mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga mudzi pozungulira pake, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pake; ndi Yowabu anakonzanso potsala pa mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamanga malo onse ozungulira, kuyambira ku matsitso ozungulira khoma. Ndipo Yowabu anakonzanso mbali ina ya mzindawu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga mudzi pozungulira pace, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pace; ndi Yoabu anakonzanso potsala pa mudzi.