1 Chronicles 11:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mphamvu za Davide zidanka zikulirakulira, chifukwa Chauta wamphamvuzonse anali naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakulakulabe, pakuti Yehova wa makamu anali naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mphamvu za Davide zinkakulirakulira chifukwa anali ndi Yehova Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakula-kulabe, pakuti Yehova wa makamu anali naye.