1 Chronicles 12:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wa 10 Yeremiya, wa 11 Makibanai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakhumi Yeremiya, wakhumi ndi chimodzi Makibanai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wakhumi anali Yeremiya ndipo Makibanai anali wa 11.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wakhumi Yeremiya, wakhumi ndi cimodzi Makibanai.