1 Chronicles 12:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwoŵa anali anthu odziŵa kugwiritsa ntchito uta. Mivi ndi miyala ankatha kuponyera dzanja lamanja kapena lamanzere. Iwoŵa anali Abenjamini, abale ake a Saulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mivi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ake a Saulo, Abenjamini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anali ndi mauta ndipo amadziwa kuponya mivi komanso miyala, ndipo amatha kuponyera dzanja lamanja kapena lamanzere. Iwo anali abale ake a Sauli ochokera ku fuko la Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mibvi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ace a Sauli, Abenjamini.