1 Chronicles 12:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zadoki mnyamata wolimba mtima adabwera ndi achibale ake 22.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Zadoki, ndiye mnyamata, ngwazi yamphamvu, ndi a nyumba ya kholo lake akulu makumi awiri mphambu awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi Zadoki, mnyamata wankhondo wolimba mtima, anabwera ndi akuluakulu 22 ochokera mʼbanja lake;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Zadoki, ndiye mnyamata, ngwazi yamphamvu, ndi a nyumba ya kholo lace, akuru makumi awiri mphambu awfri.