1 Chronicles 12:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Benjamini, abale ake a Saulo, analipo 3,000. Koma mpaka pa nthaŵi imeneyo, ambiri mwa iwowo ankaumirirabe kumatsata banja la Saulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Benjamini, abale a Saulo, zikwi zitatu; pakuti mpaka pomwepo ochuluka a iwowa anaumirira nyumba ya Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Benjamini, abale ake a Sauli analipo 3,000 ndipo ambiri anali ndi Sauli ku nyumba yake pa nthawiyi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Benjamini, abale a Sauli, zikwi zitatu; pakuti mpaka pomwepo ocuruka a iwowa anaumirira nyumba ya Sauli.