1 Chronicles 12:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A banja la Efuremu, 20,800 anthu amphamvu ndi olimba mtima, anthu omveka ku mabanja a makolo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Efuremu zikwi makumi awiri mphambu mazana asanu ndi atatu, ngwazi zamphamvu, anthu omveka m'nyumba za makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Efereimu, asilikali olimba mtima, otchuka pa mabanja awo analipo 20,800;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Efraimu zikwi makumi awiri mphambu mazana asanu ndi atatu, ngwazi zamphamvu, anthu omveka m'nyumba za makolo ao.