1 Chronicles 12:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko lahafu la Manase analipo 18,000, amene adaachita kuŵaitana kuti adzalonge nao ufumu Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo a fuko la Manase logawika pakati zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, otchulidwa maina ao kuti adzalonge Davide mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko latheka la Manase amene anawayitana kuti adzakhazikitse nawo ufumu wa Davide analipo 18,000;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo a pfuko la Manase logawika pakati zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, ochulidwa maina ao kuti adzalonge Davide mfumu.