1 Chronicles 12:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Isakara analipo atsogoleri 200 pamodzi ndi anthu ao. Atsogoleriwo ankamvetsa zinthu pa nthaŵi imeneyo, namadziŵa zimene Israele ankayenera kuchita pa nthaŵi yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israele kuzichita, akulu ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Isakara amene ankazindikira nthawi ndipo amadziwa zimene Israeli ankayenera kuchita, analipo atsogoleri 200 pamodzi ndi abale awo onse amene amawatsogolera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israyeli kuzicita, akuru ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.