1 Chronicles 12:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Zebuloni analipo 50,000 asilikali okonzekera nkhondo, okhala ndi zida zankhondo zamitundumitundu, othandiza Davide ndi mtima umodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
A Zebuloni akutuluka kukhamu, opangira nkhondo, monga mwa zida zilizonse za nkhondo, zikwi makumi asanu, akusunga malongosoledwe a nkhondo ndi mtima wosatekeseka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Zebuloni, analipo 5,000. Iwowa anali asilikali odziwa bwino nkhondo, okhala ndi zida za mtundu uliwonse, okonzekera kudzathandiza Davide ndi mtima umodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
A Zebuloni akuturuka kukhamu, opangira nkhondo, monga mwa zida ziri zonse za nkhondo, zikwi makumi asanu, akusunga malongosoledwe a nkhondo ndi mtima wosatekeseka.