1 Chronicles 12:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
A fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi fuko lahafu la Manase, kuchokera pa tsidya ilo la mtsinje wa Yordani, analipo 120,000 odziŵa kumenya nkhondo ndi zida zosiyanasiyana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi tsidya lija la Yordani a Arubeni, ndi Agadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, ndi zina zilizonse za khamu kuchita nazo nkhondo, zikwi zana limodzi ndi makumi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo kuchokera kummawa kwa Yorodani, anthu a fuko la Rubeni, Gadi ndi theka la fuko la Manase, amene anali ndi zida za mtundu uliwonse analipo 120,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi tsidya lga la Yordano a Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la: Manase logawika pakati, ndi zida: ziri zonse za khamu kucita nazo nkhondo, zikwi zana limodzi ndi makumi awiri.