1 Chronicles 12:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adakhala komweko masiku atatu pamodzi ndi Davide namadya zimene abale ao anali ataŵakonzekera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anali komweko kwa Davide masiku atatu kudya ndi kumwa, popeza abale ao anazikonzeratu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwa anakhala ndi Davide masiku atatu akudya ndi kumwa pakuti mabanja awo anawapatsa zakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anali komweko kwa Davide masiku atatu kudya ndi kumwa, popeza abale ao-anazikonzeratu.