1 Chronicles 14:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ukakamva phokoso pa nsonga za mitengo ya mkandankhukuyo, pamenepo utuluke kukamenyana nawo. Pakuti Mulungu wakutsogolera kuti ukakanthe gulu lankhondo la Afilistiwo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula kunsonga kwa mitengo ya mkandankhuku, pamenepo utulukire kunkhondo; pakuti Mulungu watulukira pamaso pako kukantha gulu la Afilisti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukakangomva phokoso pa msonga za mitengo ya mkandankhuku, mukapite kukamenyana nawo, chifukwa izi zikasonyeza kuti Mulungu ali patsogolo panu kukantha ankhondo a Afilisti.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula kunsonga kwa mitengo ya mkandankhuku, pamenepo uturukire kunkhondo; pakuti Mulungu waturukira pamaso pako kukantha gulu la Afilisti.