1 Chronicles 14:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mbiri ya Davide idawanda ku maiko onse, ndipo Ambuye adachititsa mantha anthu a mitundu yonse kuti azimuwopa Davideyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mbiri ya Davide inabuka m'maiko onse, nafikitsira Yehova kuopsa kwake pa amitundu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mbiri ya Davide inafalikira dziko lonse, ndipo Yehova anachititsa kuti mayiko ena azimuopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mbiri ya Davide inabuka m'maiko onse, nafikitsira Yehova kuopsa kwace pa amitundu onse.