1 Chronicles 15:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti simudalinyamule ndinu poyamba paja, Chauta adatikantha, chifukwa choti sitidasamale mwambo wake polinyamula.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, chifukwa cha kusalinyamula inu poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anachita chotipasula, popeza sitinamfunafuna Iye monga mwa chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza kuti inu Alevi simunalinyamule poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anatikantha. Sitinafunse momwe tikanachitira monga mmene Iyeyo anafotokozera.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, cifukwa ca kusalinyamula inu poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anacita cotipasula, popeza sitinamfunafuma Iye monga mwa ciweruzo.