1 Chronicles 15:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Alevi adasankha Hemani mwana wa Yowele, ndipo mwa abale ake adasankha Asafu mwana wa Berekiya. Mwa ana a Merari, abale ao, adasankha Etani mwana wa Kusaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Alevi anaika Hemani mwana wa Yowele, ndi a abale ake Asafu mwana wa Berekiya, ndi a ana a Merari, abale ao, Etani mwana wa Kusaya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Alevi anasankha Hemani mwana wa Yoweli; ndipo mwa abale ake anasankha Asafu mwana wa Berekiya; ndipo mwa ana a Merari, abale awo, anasankha Etani mwana wa Kusaya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Alevi anaika Hemani mwana wa Yoeli, ndi a abale ace Asafu mwana wa Berekiya, ndi a ana a Merari, abale ao, Etani mwana wa Kusaya;