1 Chronicles 15:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaniya, mtsogoleri wa Alevi poimba nyimbo, ndiye amene ankatsogolera kuimbako, poti anali katswiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Kenaniya mkulu wa Alevi anayang'anira kusenzako; anawalangiza za kusenza, pakuti anali waluso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaniya, mtsogoleri wa Alevi anali woyangʼanira mayimbidwe; uwu ndiye unali udindo wake pakuti anali waluso pa zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Kenaniya mkuru wa Alevi anayang'anira kusenzako; anawalangiza za kusenza, pakuti anali waluso.