1 Chronicles 16:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munyadire dzina lake loyera. Ikondwe mitima ya anthu amene amapembedza Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzitamandire ndi dzina lake lopatulika; mitima yao ya iwo ofuna Yehova ikondwere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyadirani dzina lake loyera; ikondwere mitima ya iwo akufunafuna Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzitamandire ndi dzina lace lopatulika; Mitima yao ya iwo ofuna Yehova ikondwere.