1 Chronicles 16:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzikumbukira ntchito zodabwitsa za Chauta, zozizwitsa zimene adachita, ndi m'mene ankaweruzira anthu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani zodabwitsa zake adazichita, zizindikiro zake, ndi maweruzo a pakamwa pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani ntchito zodabwitsa wazichita, zozizwitsa zake, ndi kuweruza kwa mʼkamwa mwake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani zodabwiza zace adazicita, Zizindikilo zace, ndi maweruzo a pakamwa pace;