1 Chronicles 16:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzikumbukira chipangano chake nthaŵi zonse, musaiŵale mpaka muyaya mau amene Iye adalamula,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani chipangano chake kosatha, mauwo anawalamulira mibadwo zikwi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakumbukira pangano lake nthawi zonse, mawu amene Iye analamula, kwa mibado miyandamiyanda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani cipangano cace kosatha, Mauwo anawalamulira mibadwo zikwi;