1 Chronicles 16:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adati, “Ndidzakupatsa dziko la Kanani, kuti likhale choloŵa chako chokhalira iweyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kunena kuti, Ndidzakupatsa iwe dziko la Kanani, gawo la cholandira chako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kwa iwe, ine ndidzapereka dziko la Kanaani monga cholowa chimene udzachilandira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kunena kuti, Ndidzakupatsa iwe dziko la Kanani, Gawo la colandira cako;