1 Chronicles 16:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anali anthu oŵerengeka, anthu osatchuka, ongokhala nao m'dzikomo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pokhala inu anthu owerengeka, inde anthu pang'ono, ndi alendo m'mwemo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ali anthu owerengeka, ochepa ndithu, komanso alendo mʼdzikomo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokhala inu anthu owerengeka, Inde anthu pang'ono, ndi alendo m'mwemo;