1 Chronicles 16:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
sadalole ndi mmodzi yemwe aŵapsinje, adalanga mafumu ena chifukwa cha anthu akewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanalole munthu awasautse; ndipo anadzudzula mafumu chifukwa cha iwowa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye sanalole munthu aliyense kuti awapondereze; chifukwa cha iwo, Iye anadzudzula mafumu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanalola munthu awasautse; Ndipo anadzudzula mafumu cifukwa ca iwowa;