1 Chronicles 16:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbirani Chauta, inu anthu a dziko lonse lapansi. Lengezani tsiku ndi tsiku za m'mene Iye adapulumutsira anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muimbireni Yehova, inu dziko lonse lapansi, lalikirani chipulumutso chake tsiku ndi tsiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imbirani Yehova, dziko lonse lapansi; lalikani za chipulumutso chake tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Myimbireni Yehova, inu dziko lonse lapansi, Lalikirani cipulumutso cace tsiku ndi tsiku,