1 Chronicles 16:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ngwamkulu, ngwoyenera kumtamanda kwambiri, ngwoyenera kumuwopa kupambana milungu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova ali wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ayenera amuope koposa milungu yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kwambiri kumutamanda; Iyeyo ayenera kuopedwa kuposa milungu yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova ali wamkuru, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; Ayenera amuope koposa milungu yonse.