1 Chronicles 16:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja milungu ya anthu a mitundu ina ndi mafano chabe, koma Chauta ndiye adalenga zakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti milungu ya mitundu ya anthu ndiyo mafano; koma Yehova analenga zakumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi mafano wopanda pake, koma Yehova analenga kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti milungu ya mitundu ya anthu ndiyo mafano; Koma Yehova analenga zakumwamba.